Malo olembetsera kalembera wachibwereza atsegulidwa kuyambira nthawi ya 8:00 m’mawa uno. Kafikeni ku malo a kalembera omwe muli nawo pafupi kuti mukalembetse mukawundula wa voti ngati muli kuma khonsolo awa; 1. Chigawo chaku mpoto: Mzimba. 2. Chigawo chapakati Lilongwe City, Lilongwe. 3. Chigawo chakumwera: Mangochi, Mwanza, Chikwawa, Nsanje #KalemberaWaChisankho #ChisankhoCha2025
Read More