Malo olembetsera kalembera wachibwereza atsegulidwa kuyambira nthawi ya 8:00 m’mawa uno. Kafikeni ku malo a kalembera omwe muli nawo pafupi kuti mukalembetse mukawundula wa voti ngati muli kuma khonsolo awa;
1. Chigawo chaku mpoto:
Mzimba.
2. Chigawo chapakati
Lilongwe City, Lilongwe.
3. Chigawo chakumwera:
Mangochi,
Mwanza,
Chikwawa,
Nsanje
#KalemberaWaChisankho #ChisankhoCha2025
