Ululani nkhanza zomwe ana akukumana nazo poimba foni ku Tithandizane National Child Helpline pa 116 ndipo mukhozanso kuulula nkhanza zochitika chifukwa wina ndi mwamuna kapena mkazi poimba foni pa 5600. Kumbukirani kuti nambalazi ndizaulere.

0Shares

Leave a Comment