Dziwani za matenda a Mpox Mawu Oyamba Unduna wa za Umoyo ukulengeza kuti kwadza matenda otchedwa Mpox omwe avuta m’mayiko ambiri ku m’mwera kwa Africa. Anthu ambiri adwala komanso kumwalira ndi matendawa. Bungwe la za Umoyo pa dziko lonse la World Health Organisation lidalengeza pa 14 August, 2024 kuti mliri wa matendawa tsopano ndi chiopsezo…
Read More