Tiyeni titenge mbali pothetsa nkhanza kwa amai ndi ana poneneza anthu omwe amachita nkhanzazi poyimba foni mwaulere pa 5600 #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreMuvi oyang’anira suchedwa kulowa mmaso. Nkhaza zimabweretsa mabvuto osiyanasiyana. Tiyeni tiulure nkhazazi kwa adindo. Kapena kuyimba foni mwaulere pa 5600. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreNkhanza tikazilekelera zimabala mavuto aakulu. Tiyeni tisachitire ena nkhanza, koma tikondane ndikutetezana wina ndi nzake. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreTiyeni tiwazindikiritse ana anthu nkhanza zomwe angakumanenazo ndikuwalimbikitsa kuti adziulura akachitilidwa nkhanzazi. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreNkhanza zimabwezera chitikuko pambuyo. Atsogoleri ndi udindo wathu kuthetsa nkhanza zochitika chifukwa wina ndi mamuna kapena mkazi. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreNane Ndimafuna ndizakhale pomwe mulipo. Musandichite nkhanza koma ndithandizeni kukwaniritsa maloto anga. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAdindo, limbikitsani ntchito yoteteza ufulu wa amayi ndi ana munthawi ya ngozi zogwa mwadzidzi. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreMakolo onetsetsani kuti mukuwamasukira ana anu kunkhani zogonana kuwopa kuuzidwa zosayenera ndi amzawo. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreTiyeni tileke kupondeleza amayi pantchito zamalonda kuti tichepetse kudalira komwe kumadzetsa nkhanza. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read More