Achinyamata tiyeni tisachitirane Nkhanza koma titetezane kunkhanza zomwe timakumana nazo Tsiku ndi Tsiku. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAdindo, tiyeni titenge gawo polimbikitsa ufulu wa amayi pantchito, powateteza kunkhanza zosiyanasiyana. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAtsogoleri, tiyeni tisagwiritse ntchito udindo ngati chida chochitira nkhanza amayi ndi asungwana. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read More