Chikondi sinkhondo; achinyamata ngati okondedwa wanu akukuchitani nkhanza kaneneni kwa adindo a mdera lanu. Mukhozanso kuulura nkhanza zotere poimba foni mwaulere pa 5600.
#SDG5 #16DaysofActivism #endGBV

0Shares

Leave a Comment