Tiyeni tilemekeze ufulu wa amayi ndi atsikana. Tisaikire ndemanga zonyoza/zosakhala bwino pazithuzi zomwe zayikidwa pa masamba a mchezo.
#SDG5 #16DaysofActivism #endGBV

0Shares

Leave a Comment