Nkhanza zimabwezera chitikuko pambuyo. Atsogoleri ndi udindo wathu kuthetsa nkhanza zochitika chifukwa wina ndi mamuna kapena mkazi. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MorePlease follow the link to read or download YONECO VOICE-Monthly Newsletter-December 2022
Read MoreNane Ndimafuna ndizakhale pomwe mulipo. Musandichite nkhanza koma ndithandizeni kukwaniritsa maloto anga. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAdindo, limbikitsani ntchito yoteteza ufulu wa amayi ndi ana munthawi ya ngozi zogwa mwadzidzi. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreMakolo onetsetsani kuti mukuwamasukira ana anu kunkhani zogonana kuwopa kuuzidwa zosayenera ndi amzawo. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreTiyeni tileke kupondeleza amayi pantchito zamalonda kuti tichepetse kudalira komwe kumadzetsa nkhanza. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreBanja sinkhondo, ulurani nkhanza zomwe okondedwa anu akukuchitirani poimba foni mwaulere pa 5600. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read More“I easily engage and reach out to my fellow young people with Sexual Reproductive Health and Rights (SRHR) information through social media. As a Peer Educator, this approach has helped me to forget about issues of mobility which used to prevent me from reaching many young people in my area which has over 14 small…
Read MoreTiyeni tilemekeze ufulu wa amayi ndi atsikana. Tisaikire ndemanga zonyoza/zosakhala bwino pazithuzi zomwe zayikidwa pa masamba a mchezo. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreOn 28 November, 2022, the Director of Agriculture Planning Services in the Ministry of Agriculture and Food Security, Rodwel Mzonde, officially launched Sustainable Land Management (SAMALA) Project at Luwerezi in Mzimba district. The five-year project will be implemented by Total Landcare, YONECO and World Agroforestry Centre with support from the Government of Flanders and Irish…
Read More