Banja sinkhondo, ulurani nkhanza zomwe okondedwa anu akukuchitirani poimba foni mwaulere pa 5600. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreTiyeni tilemekeze ufulu wa amayi ndi atsikana. Tisaikire ndemanga zonyoza/zosakhala bwino pazithuzi zomwe zayikidwa pa masamba a mchezo. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreChikondi sinkhondo; achinyamata ngati okondedwa wanu akukuchitani nkhanza kaneneni kwa adindo a mdera lanu. Mukhozanso kuulura nkhanza zotere poimba foni mwaulere pa 5600. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAchinyamata tiyeni tisachitirane Nkhanza koma titetezane kunkhanza zomwe timakumana nazo Tsiku ndi Tsiku. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAdindo, tiyeni titenge gawo polimbikitsa ufulu wa amayi pantchito, powateteza kunkhanza zosiyanasiyana. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreAtsogoleri, tiyeni tisagwiritse ntchito udindo ngati chida chochitira nkhanza amayi ndi asungwana. #SDG5 #16DaysofActivism #endGBV
Read MoreYouth Net and Counselling (YONECO) is a local NGO that is committed to empowering youth, women and children, preventing the spread of HIV infection, mitigating the impact of AIDS, promoting democracy and human rights and conducting research on youth, women and children development. YONECO vision is a self-reliant, healthy and resilient society that respects democratic…
Read More